Maupangiri pakuwunika ndi kuyezetsa COVID-19
Kuyezetsa COVID-19 kungakuthandizeni kudziwa ngati muli ndi COVID-19 kuti mutha kusankha zochita, monga kupeza mankhwala kuchepetsa chiopsezo cha matenda aakulu ndi kuchitapo kanthu kuti muchepetse mwayi wanu wofalitsa kachilomboka kwa ena.